Genesis 31:22 - Buku Lopatulika22 Tsiku lachitatu anamuuza Labani kuti Yakobo wathawa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 Tsiku lachitatu anamuuza Labani kuti Yakobo wathawa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 Patapita masiku atatu, Labani adamva kuti Yakobe adathaŵa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 Patapita masiku atatu, Labani anawuzidwa kuti Yakobo wathawa. Onani mutuwo |