Genesis 31:20 - Buku Lopatulika20 Ndipo Yakobo anathawa kwa Labani Mwaramu mobisika, m'mene sanamuuze iye kuti analinkuthawa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 Ndipo Yakobo anathawa kwa Labani Mwaramu mobisika, m'mene sanamuuze iye kuti analinkuthawa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Motero Yakobe adampusitsa Labani Mwaramu uja posamuuza kuti akuchoka. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 Komanso nthawi iyi nʼkuti Yakobo atamunamiza Labani Mwaramu posamuwuza zoona kuti afuna kuthawa. Onani mutuwo |