Genesis 31:16 - Buku Lopatulika16 Chifukwa kuti chuma chonse Mulungu anachichotsa kwa atate wathu ndi chathu ndi cha ana athu; tsono, zonse wakunenera iwe Mulungu, uchite. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Chifukwa kuti chuma chonse Mulungu anachichotsa kwa atate wathu ndi chathu ndi cha ana athu; tsono, zonse wakunenera iwe Mulungu, uchite. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Chuma chonse chimene Mulungu wachotsa kwa bambo wathu, ndi chathu ndi cha ana athu. Chitani zimene Mulungu wakuuzani.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Chuma chonse chimene Mulungu walanda abambo athu, ndi chathu ndi ana athu. Tsono inu chitani zimene Mulungu wakuwuzani.” Onani mutuwo |