Genesis 31:14 - Buku Lopatulika14 Ndipo Rakele ndi Leya anayankha, nati kwa iye, Kodi tili nalonso gawo kapena cholowa m'nyumba ya atate wathu? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Ndipo Rakele ndi Leya anayankha, nati kwa iye, Kodi tili nalonso gawo kapena cholowa m'nyumba ya atate wathu? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Rakele ndi Leya adayankha kuti, “Palibe chomwe chatitsalira ife kwa bambo wathu choti chikhale choloŵa chathu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Pamenepo Rakele ndi Leya anayankha, “Kodi ngati ife tilinso ndi gawo ngati cholowa pa chuma cha abambo athu? Onani mutuwo |