Genesis 30:17 - Buku Lopatulika17 Ndipo Mulungu anamvera Leya, ndipo anatenga pakati, nambalira Yakobo mwana wamwamuna wachisanu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Ndipo Mulungu anamvera Leya, ndipo anatenga pakati, nambalira Yakobo mwana wamwamuna wachisanu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Mulungu adamva pemphero la Leya, choncho adatenga pathupi, namubalira Yakobe mwana wamwamuna wachisanu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Mulungu anamva pemphero la Leya ndipo anatenga pathupi nabalira Yakobo mwana wa mwamuna wachisanu. Onani mutuwo |