Genesis 29:27 - Buku Lopatulika27 Umalize sabata lake la uyu, ndipo ndidzakupatsa uyonso chifukwa cha utumiki umene udzanditumikirawo kuonjezera zaka zina zisanu ndi ziwiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201427 Umalize sabata lake la uyu, ndipo ndidzakupatsa uyonso chifukwa cha utumiki umene udzanditumikirawo kuonjezera zaka zina zisanu ndi ziwiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa27 Dikira, yamba watsiriza mlungu uno wa chikondwerero chaukwati, kenaka ndidzakupatsa Rakele, komatu udzandigwiriranso ntchito zaka zina zisanu ndi ziŵiri.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero27 Yamba watsiriza sabata ya chikondwerero cha ukwati wa Leya; kenaka ndidzakupatsanso Rakele. Koma udzayenera kundigwirira ntchito zaka zisanu ndi ziwiri.” Onani mutuwo |