Genesis 29:26 - Buku Lopatulika26 Ndipo Labani anati, Satero kwathu kuno, kupatsa wamng'ono asanapatse wamkulu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201426 Ndipo Labani anati, Satero kwathu kuno, kupatsa wamng'ono asanapatse wamkulu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa26 Labani adayankha kuti, “Si mwambo wathu kuno kukwatitsa wamng'ono, mkulu wake asanakwatiwe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero26 Labani anayankha, “Si mwambo wathu kuno kupereka wamngʼono ku banja, wamkulu asanakwatiwe. Onani mutuwo |