Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Genesis 29:23 - Buku Lopatulika

23 Ndipo panali madzulo Labani anatenga Leya mwana wake wamkazi, nadza naye kwa Yakobo, ndipo iye analowa kwa mkaziyo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

23 Ndipo panali madzulo Labani anatenga Leya mwana wake wamkazi, nadza naye kwa Yakobo, ndipo iye analowa kwa mkaziyo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

23 Koma usiku umenewo Labani adatenga Leya m'malo mwa Rakele nampatsa Yakobe, ndipo Yakobe adaloŵana ndi Leya.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

23 Koma pokwana usiku, Labani anatenga mwana wake wamkazi Leya namupatsa Yakobo, ndipo Yakobo anagona naye.

Onani mutuwo Koperani




Genesis 29:23
6 Mawu Ofanana  

Ndipo anati kwa mnyamata, Munthuyo ndani amene ayenda m'munda kukomana ndi ife? Mnyamatayo ndipo anati, Uyo ndi mbuyanga: chifukwa chake namwali anatenga chophimba chake nadziphimba.


Ndipo Labani anasonkhanitsa anthu onse a kumeneko nakonzera madyerero.


Ndipo Labani anampatsa mwana wake wamkazi Leya Zilipa mdzakazi wake kuti akhale mdzakazi wa Leya.


Kodi satiyesa ife alendo? Chifukwa anatigulitsa ife, nathanso kuononga ndalama zathu.


Musakhulupirira bwenzi, musatama bwenzi loyanja; usamtsegulire pakhomo pakamwa pako, ngakhale kwa iye wogona m'fukato mwako.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa