Genesis 29:19 - Buku Lopatulika19 Ndipo anati Labani, Kuli kwabwino kuti ndimpatse iwe osampatsa kwa mwamuna wina; ukhalebe ndi ine. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Ndipo anati Labani, Kuli kwabwino kuti ndimpatse iwe osampatsa kwa mwamuna wina; ukhalebe ndi ine. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Choncho Labani adati, “Ndi bwino kwambiri kuti Rakeleyu ndipatse iwe, osati munthu wina aliyense. Khala ndi ine.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Labani anati, “Kuli bwino kuti ndimupereke kwa iwe ameneyu kusiyana ndi munthu wina. Khala ndi ine kuno.” Onani mutuwo |