Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Genesis 29:16 - Buku Lopatulika

16 Ndipo Labani anali ndi ana aakazi awiri, dzina la wamkulu ndi Leya, dzina la wamng'ono ndi Rakele.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

16 Ndipo Labani anali ndi ana akazi awiri, dzina la wamkulu ndi Leya, dzina la wamng'ono ndi Rakele.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

16 Labani anali ndi ana aakazi aŵiri, wamkulu Leya, wamng'ono Rakele.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

16 Tsono Labani anali ndi ana aakazi awiri; dzina la wamkulu linali Leya, ndipo dzina la wamngʼono linali Rakele.

Onani mutuwo Koperani




Genesis 29:16
10 Mawu Ofanana  

Ndipo Labani anati kwa Yakobo, Chifukwa iwe ndiwe mbale wanga, kodi udzanditumikira ine kwachabe? Undiuze ine, malipiro ako adzakhala otani?


Maso a Leya anali ofooka, koma Rakele anali wokoma thupi ndi wokongola.


Ndipo Leya anatenganso pakati nambalira Yakobo mwana wamwamuna wachisanu ndi chimodzi.


Ndipo Yakobo anatumiza naitana Rakele ndi Leya adze kubusa ku zoweta zake,


Ndipo anaika adzakazi ndi ana ao patsogolo, ndi Leya ndi ana ake pambuyo pao, ndi Rakele ndi Yosefe pambuyo pa onse.


ana aamuna a Leya: ndiwo Rubeni mwana woyamba wa Yakobo, ndi Simeoni ndi Levi, ndi Yuda, ndi Zebuloni, ndi Isakara;


Amenewo ndi ana aamuna a Leya, amene anambalira Yakobo ku Padanaramu, pamodzi ndi mwana wamkazi wake Dina; ana aamuna ndi aakazi onse ndiwo anthu makumi atatu kudza atatu.


pamenepo anaika Abrahamu ndi Sara mkazi wake; pamenepo anaika Isaki ndi Rebeka mkazi wake: pamenepo ndinaika Leya:


Pamenepo anthu onse anali kuchipata, ndi akulu, anati, Tili mboni ife. Yehova achite kuti mkazi wakulowayo m'nyumba mwako ange Rakele ndi Leya, amene anamanga nyumba ya Israele, iwo awiri; nuchite iwe moyenera mu Efurata, numveke mu Betelehemu;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa