Genesis 29:14 - Buku Lopatulika14 Ndipo Labani anati kwa iye, Eetu, iwe ndiwe fupa langa ndi thupi langa. Ndipo anakhala naye nthawi ya mwezi umodzi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Ndipo Labani anati kwa iye, Etu, iwe ndiwe fupa langa ndi thupi langa. Ndipo anakhala naye nthawi ya mwezi umodzi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Apo Labani adamuuza kuti, “Inde, zoonadi, iwe ndiwe mbale wanga weniweni.” Yakobe adakhala kumeneko mwezi wathunthu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Ndipo, Labani anati kwa iye, “Iwe ndiwe ndithu fupa ndi mnofu wanga.” Yakobo anakhala ndi Labani mwezi umodzi. Onani mutuwo |