Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Genesis 25:24 - Buku Lopatulika

24 Atatha masiku ake akubala, taonani, amapasa anali m'mimba mwake.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

24 Atatha masiku ake akubala, taonani, amapasa anali m'mimba mwake.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

24 Nthaŵi yakuti achire itakwana, Rebeka adabala mapasa.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

24 Pamene nthawi inakwana yakuti abeleke, Rebeka anaberekadi mapasa.

Onani mutuwo Koperani




Genesis 25:24
7 Mawu Ofanana  

Yehova ndipo anati kwa iye, Mitundu iwiri ili m'mimba mwako, magulu awiri a anthu adzatuluka m'mimba mwako; gulu lina lidzapambana mphamvu ndi linzake; wamkulu adzakhala kapolo wa wamng'ono.


Ndipo woyamba anabadwa wofiira, mwake monse monga malaya aubweya; ndipo anamutcha dzina lake Esau.


Mibadwo ya Esau (ndiye Edomu) ndi iyi:


Ndipo panali nthawi ya kubala kwake, taonani, amapasa anali m'mimba mwake.


Ndipo Abrahamu anabala Isaki. Ana a Isaki: Esau, ndi Israele.


Musamanyansidwa naye Mwedomu, popeza ndiye mbale wanu; musamanyansidwa naye Mwejipito, popeza munali alendo m'dziko lake.


Ndi kwa Isaki ndinapatsa Yakobo ndi Esau, ndipo ndinampatsa Esau phiri la Seiri likhale lakelake; koma Yakobo ndi ana ake anatsikira kunka ku Ejipito.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa