Genesis 25:22 - Buku Lopatulika22 Ndipo ana analimbana m'kati mwake: ndipo iye anati, Ngati chotero, ine ndikhala ndi moyo bwanji? Ndipo ananka kukafunsa kwa Yehova. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 Ndipo ana analimbana m'kati mwake: ndipo iye anati, Ngati chotero, ine ndikhala ndi moyo bwanji? Ndipo ananka kukafunsa kwa Yehova. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 Koma pamene ana aŵiriwo anayamba kulimbana m'mimba mwake, adati, “Ngati umu ndimo m'mene zikhalire zinthu, ndikhaliranji ndi moyo?” Ndipo adakafunsa Chauta kuti amuyankhe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 Koma pamene anawo amalimbana mʼmimba mwake, iye anati, “Bwanji zikundichitikira zoterezi?” Choncho anapita kukafunsa kwa Yehova. Onani mutuwo |