Genesis 25:17 - Buku Lopatulika17 Zaka za moyo wa Ismaele ndi izi: zaka zana limodzi kudza makumi atatu ndi zisanu ndi ziwiri: ndipo iye anamwalira, natengedwa akhale ndi a mtundu wake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Zaka za moyo wa Ismaele ndi izi: zaka zana limodzi kudza makumi atatu ndi zisanu ndi ziwiri: ndipo iye anamwalira, natengedwa akhale ndi a mtundu wake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 (Ismaele anali wa zaka 137 pa nthaŵi imene ankamwalira, ndipo adaikidwa m'manda.) Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Ismaeli anakhala ndi moyo zaka 137. Iye anamwalira ndipo anakakhala ndi anthu a mtundu wake. Onani mutuwo |