Genesis 25:16 - Buku Lopatulika16 ana a Ismaele ndi awa: maina ao m'midzi yao, m'misasa yao ndi awa: akalonga khumi ndi awiri m'mitundu yao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 ana a Ismaele ndi awa: maina ao m'midzi yao, m'misasa yao ndi awa: akalonga khumi ndi awiri m'mitundu yao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Ameneŵa ndiwo ana a Ismaele malinga ndi midzi yao ndiponso zigono zao. Anali mafumu khumi ndi aŵiri a mafuko osiyana. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Amenewa ndi ana a Ismaeli ndi mayina awo monga mwa midzi ndi misasa yawo. Anali olamulira mafuko khumi ndi awiri. Onani mutuwo |