Genesis 1:15 - Buku Lopatulika15 Zikhale zounikira m'thambo la kumwamba, kuti ziunikire padziko lapansi; ndipo kunatero. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Zikhale zounikira m'thambo la kumwamba, kuti ziunikire pa dziko lapansi: ndipo kunatero. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Miyuni imeneyi ikhale ku thambo ndi kumaunikira dziko lapansi,” ndipo zidachitikadi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 zikhale kuthambo kuti ziwunikire pa dziko lapansi. Ndipo zinachitikadi.” Onani mutuwo |