Ezara 8:9 - Buku Lopatulika9 Wa ana a Yowabu, Obadiya mwana wa Yehiyele; ndi pamodzi naye amuna mazana awiri mphambu khumi kudza asanu ndi atatu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Wa ana a Yowabu, Obadiya mwana wa Yehiyele; ndi pamodzi naye amuna mazana awiri mphambu khumi kudza asanu ndi atatu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Obadiya, mwana wa Yehiyele, wa fuko la Yowabu. Pamodzi ndi iyeyo panali anthu 218. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Obadiya, mwana wa Yehieli wa fuko la Yowabu. Pamodzi naye panalinso anthu 218. Onani mutuwo |