Ezara 8:5 - Buku Lopatulika5 Wa ana a Sekaniya, mwana wa Yahaziele; ndi pamodzi naye amuna mazana atatu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Wa ana a Sekaniya, mwana wa Yahaziele; ndi pamodzi naye amuna mazana atatu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Sekaniya, mwana wa Yahaziele, wa fuko la Zatu. Pamodzi ndi iyeyo panali anthu 300. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Sekaniya, mwana wa Yahazieli wa fuko la Zatu. Pamodzi ndi iyeyu panalembedwanso anthu 300. Onani mutuwo |