Ezara 8:4 - Buku Lopatulika4 Wa ana a Pahatimowabu, Eliehoenai mwana wa Zerahiya; ndi pamodzi naye amuna mazana awiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Wa ana a Pahatimowabu, Eliehoenai mwana wa Zerahiya; ndi pamodzi naye amuna mazana awiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Eliehoenai, mwana wa Zerahiya, wa fuko la Pahatimowabu. Pamodzi ndi iyeyo panali anthu 200. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Elihunai mwana wa Zerahiya, wa fuko la Pahati-Mowabu. Pamodzi ndi iyeyu panalinso anthu ena 400. Onani mutuwo |