Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Ezara 8:3 - Buku Lopatulika

3 Wa ana a Sekaniya, wa ana a Parosi, Zekariya; ndi pamodzi naye, powawerenga monga mwa chibadwidwe chao, amuna zana limodzi mphambu makumi asanu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

3 Wa ana a Sekaniya, wa ana a Parosi, Zekariya; ndi pamodzi naye, powawerenga monga mwa chibadwidwe chao, amuna zana limodzi mphambu makumi asanu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

3 Hatusi, mwana wa Sekaniya, wa fuko la Davide. Zekariya, wa fuko la Parosi. Iyeyu adalembedwa pamodzi ndi anthu ena okwanira 150.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

3 mwana wa Sekaniya wa fuko la Davide; Zekariya wa fuko la Parosi. Pamodzi ndi iyeyu panalembedwa anthu ena 150;

Onani mutuwo Koperani




Ezara 8:3
7 Mawu Ofanana  

Ndi ana a Hananiya: Pelatiya, ndi Yesaya, ana a Refaya, ana a Arinani, ana a Obadiya, ana a Sekaniya.


Ndi mwana wa Sekaniya: Semaya; ndi ana a Semaya: Hatusi, ndi Igala, ndi Bariya, ndi Neariya, ndi Safati; asanu ndi mmodzi.


Ndi Aisraele a ana a Parosi: Ramiya, ndi Iziya, ndi Matikiya, ndi Miyamini, ndi Eleazara, ndi Malikiya, ndi Benaya.


ana a Parosi, zikwi ziwiri ndi zana limodzi mphambu makumi asanu ndi awiri kudza awiri.


Wa ana a Pahatimowabu, Eliehoenai mwana wa Zerahiya; ndi pamodzi naye amuna mazana awiri.


Akulu a anthu: Parosi, Pahatimowabu, Elamu, Zatu, Bani,


ana a Parosi zikwi ziwiri mphambu zana limodzi kudza makumi asanu ndi awiri.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa