Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Ezara 8:13 - Buku Lopatulika

13 Ndi a ana otsiriza a Adonikamu, maina ao ndiwo Elifeleti, Yeiyele, ndi Semaya; ndi pamodzi nao amuna makumi asanu ndi limodzi.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

13 Ndi a ana otsiriza a Adonikamu, maina ao ndiwo Elifeleti, Yeiyele, ndi Semaya; ndi pamodzi nao amuna makumi asanu ndi limodzi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

13 Atsogoleri a fuko la Adonikamu, anthu amene adabwera pambuyo pake, anali Elifeleti, Yeiyele ndi Semaya, ndipo pamodzi ndi iwowo panali anthu 60.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

13 Atsogoleri a fuko la Adonikamu, anthu amene anabwera pambuyo pake mayina awo anali Elifeleti, Yeiyeli ndi Semaya. Pamodzi ndi iwowa panalinso anthu 60.

Onani mutuwo Koperani




Ezara 8:13
4 Mawu Ofanana  

Ana a Adonikamu, mazana asanu ndi limodzi mphambu makumi asanu ndi limodzi kudza asanu ndi mmodzi.


Ndi wa ana a Azigadi, Yohanani mwana wa Hakatani; ndi pamodzi naye amuna zana limodzi mphambu khumi limodzi.


Ndi wa ana a Bigivai, Utai ndi Zakuri, ndi pamodzi nao amuna makumi asanu ndi awiri.


Ana a Adonikamu, mazana asanu ndi limodzi mphambu makumi asanu ndi limodzi, kudza asanu ndi awiri.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa