Ezara 8:12 - Buku Lopatulika12 Ndi wa ana a Azigadi, Yohanani mwana wa Hakatani; ndi pamodzi naye amuna zana limodzi mphambu khumi limodzi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Ndi wa ana a Azigadi, Yohanani mwana wa Hakatani; ndi pamodzi naye amuna zana limodzi mphambu khumi limodzi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Yohanani, mwana wa Hakatani, wa fuko la Azigadi. Pamodzi ndi iyeyo panali anthu 110. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Yohanani, mwana wa Hakatani wa fuko la Azigadi. Pamodzi naye panalinso anthu 110. Onani mutuwo |