Ezara 8:11 - Buku Lopatulika11 Ndi wa ana a Bebai, Zekariya mwana wa Bebai; ndi pamodzi naye amuna makumi awiri mphambu asanu ndi atatu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Ndi wa ana a Bebai, Zekariya mwana wa Bebai; ndi pamodzi naye amuna makumi awiri mphambu asanu ndi atatu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Zekariya, mwana wa Bebai, wa fuko la Bebai. Pamodzi ndi iyeyo panali anthu 28. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Zekariya, mwana wa Bebai wa fuko la Babai. Pamodzi naye analembedwanso anthu 28. Onani mutuwo |