Ezara 8:10 - Buku Lopatulika10 Ndi wa ana a Selomiti, mwana wa Yosofiya; ndi pamodzi naye amuna zana limodzi mphambu makumi asanu ndi limodzi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Ndi wa ana a Selomiti, mwana wa Yosofiya; ndi pamodzi naye amuna zana limodzi mphambu makumi asanu ndi limodzi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Selomiti, mwana wa Yosofiya, wa fuko la Bani. Pamodzi ndi iyeyo panali anthu 160. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Selomiti mwana wa Yosifiya wa fuko la Bani. Pamodzi ndi iyeyu panalinso anthu 160. Onani mutuwo |