Ezara 6:4 - Buku Lopatulika4 ndi mipambo itatu ya miyala yaikulu, ndi mpambo wa mitengo yatsopano; nalipidwe ndalama zochokera kunyumba ya mfumu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 ndi mipambo itatu ya miyala yaikulu, ndi mpambo wa mitengo yatsopano; nalipidwe ndalama zochokera kunyumba ya mfumu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Mudzamange mizere itatu ya miyala yaikulu ndi mzere umodzi wa matabwa. Ndalama zake zolipirira ntchitoyo zichokere m'thumba lachifumu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Mumange mizere itatu ya miyala yayikulu ndi mzere umodzi wa matabwa, ndalama zake zolipirira ntchitoyo zichokere mʼthumba la ufumu. Onani mutuwo |