Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Ezara 6:2 - Buku Lopatulika

2 Napeza ku Ekibatana m'nyumba ya mfumu m'dera la Mediya, mpukutu, ndi m'menemo munalembedwa motere, chikhale chikumbutso:

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

2 Napeza ku Ekibatana m'nyumba ya mfumu m'dera la Mediya, mpukutu, ndi m'menemo munalembedwa motere, chikhale chikumbutso:

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

2 Tsono ku Ekibatana, likulu la dziko la Mediya, kudapezeka mpukutu m'mene mudaalembedwa kuti, “Chikumbutso.” Mau ake anali aŵa:

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

2 Ndipo ku Ekibatana, likulu la dera la Mediya, kunapezeka mpukutu mmene munalembedwa kuti, Chikumbutso:

Onani mutuwo Koperani




Ezara 6:2
3 Mawu Ofanana  

Chaka chachisanu ndi chinai cha Hoseya mfumu ya Asiriya analanda Samariya, natenga Aisraele andende, kunka nao ku Asiriya; nawakhalitsa mu Hala, ndi mu Habori, ku mtsinje wa Gozani, ndi m'mizinda ya Amedi.


Ndipo tsono chikakomera mfumu, munthu asanthule m'nyumba ya chuma cha mfumu ili komwe ku Babiloni, ngati nkuterodi, kuti Kirusi mfumu analamulira kuti azimanga nyumba iyi ya Mulungu ku Yerusalemu; ndipo mfumu ititumizire mau omkomera pa chinthuchi.


pamenepo ndinati, Taonani, ndafika, (Pamutu pake pa buku palembedwa za Ine) kudzachita chifuniro chanu, Mulungu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa