Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Ezara 5:9 - Buku Lopatulika

9 Pamenepo tinafunsa akulu aja ndi kutere nao, Anakulamulirani ndani kumanga nyumba iyi, ndi kutsiriza khoma ili?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

9 Pamenepo tinafunsa akulu aja ndi kutere nao, Anakulamulirani ndani kumanga nyumba iyi, ndi kutsiriza khoma ili?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

9 Tsono tidaŵafunsa atsogoleriwo kuti, ‘Kodi adakulamulani ndani kuti mumange Nyumba imeneyi ndi kutsiriza makoma ake?’

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

9 Ndipo tinawafunsa atsogoleriwo kuti, “Anakulolezani kuti mumangenso Nyumbayi ndi kutsiriza makoma ake ndani?”

Onani mutuwo Koperani




Ezara 5:9
4 Mawu Ofanana  

Adziwe mfumu kuti, Ayuda adakwerawo ochokera kwanu atifikira ife ku Yerusalemu, alikumanga mzinda uja wopanduka ndi woipa, alikutsiriza malinga ake, nalumikiza maziko ake.


Tinawafunsanso maina ao, kukudziwitsani, kuti tilembere maina a anthu akuwatsogolera.


Adziwe mfumu kuti ife tinamuka kudziko la Yuda, kunyumba ya Mulungu wamkulu, yomangidwa ndi miyala yaikulu, ndi kuikidwa mitengo pamakoma, ndipo inachitika mofulumira ntchitoyi, ndipo inayenda bwino m'dzanja mwao.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa