Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Ezara 5:7 - Buku Lopatulika

7 anatumiza kalata kwa iyeyo m'menemo munalembedwa motere, kwa Dariusi mfumu, mtendere wonse.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

7 anatumiza kalata kwa iyeyo m'menemo munalembedwa motere, kwa Dariusi mfumu, mtendere wonse.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

7 Adalemba kuti, “Kwa mfumu Dariusi, ulamuliro wanu ukhale ndi mtendere wonse.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

7 Analemba kalatayo motere: Kwa mfumu Dariyo: Mukhale ndi mtendere wonse.

Onani mutuwo Koperani




Ezara 5:7
8 Mawu Ofanana  

Mfumu nibweza mau kwa Rehumu chiwinda cha malamulo, ndi kwa Simisai mlembi, ndi kwa anzao otsala okhala mu Samariya, ndi otsala tsidya lino la mtsinjewo, Moni, ndi nthawi yakuti.


Zolembedwa m'kalata amene Tatenai kazembe wa tsidya lino la mtsinjewo, ndi Setari-Bozenai, ndi anzake Afarisikai, okhala tsidya lino la mtsinje, anatumiza kwa Dariusi mfumu,


Adziwe mfumu kuti ife tinamuka kudziko la Yuda, kunyumba ya Mulungu wamkulu, yomangidwa ndi miyala yaikulu, ndi kuikidwa mitengo pamakoma, ndipo inachitika mofulumira ntchitoyi, ndipo inayenda bwino m'dzanja mwao.


Anayankha, nati kwa mfumu Nebukadinezara, Mfumu, mukhale ndi moyo chikhalire.


Mfumu Nebukadinezara, kwa anthu mitundu ya anthu, ndi a manenedwe okhala padziko lonse lapansi: Mtendere uchulukire inu.


Pamenepo Daniele anati kwa mfumu, Mfumu, mukhale ndi moyo chikhalire.


Mtendere ndikusiyirani inu, mtendere wanga ndikupatsani; Ine sindikupatsani inu monga dziko lapansi lipatsa. Mtima wanu usavutike, kapena usachite mantha.


Ndipo Ambuye wa mtendere yekha atipatse ife mtendere nthawi zonse, monsemo. Ambuye akhale ndi inu nonse.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa