Ezara 5:4 - Buku Lopatulika4 Nanena naonso motere, Maina ao a anthu omanga chimangidwe ichi ndiwo ayani? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Nanena naonso motere, Maina ao a anthu omanga chimangidwe ichi ndiwo ayani? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Adaŵafunsanso kuti, “Kodi anthu amene akumanga Nyumba imeneyiŵa, maina ao ndani?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Anawafunsanso kuti, “Kodi anthu amene akumanga nyumbayi mayina awo ndani?” Onani mutuwo |