Ezara 5:10 - Buku Lopatulika10 Tinawafunsanso maina ao, kukudziwitsani, kuti tilembere maina a anthu akuwatsogolera. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Tinawafunsanso maina ao, kukudziwitsani, kuti tilembere maina a anthu akuwatsogolera. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Tidaŵafunsanso maina ao, kuti tikalemba maina a atsogoleri ao, tidzakudziŵitseni. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Tinawafunsanso mayina a atsogoleri awo, kuti tikalemba mayina atsogoleriwo tidzakudziwitseni kuti muwadziwe. Onani mutuwo |