Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Ezara 4:8 - Buku Lopatulika

8 Rehumu chiwinda cha malamulo, ndi Simisai mlembi, analemba kalata kwa mfumu Arita-kisereksesi, wakutsutsana naye Yerusalemu motere:

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

8 Rehumu chiwinda cha malamulo, ndi Simisai mlembi, analemba kalata kwa mfumu Arita-kisereksesi, wakutsutsana naye Yerusalemu motere:

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

8 Kenaka Rehumu Bwanamkubwa ndi Simisai mlembi wake, nawonso adalemba yao kalata kwa mfumu Arita-kisereksesi yoneneza anthu a ku Yerusalemu. Adalemba motere:

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

8 Rehumu mkulu wankhondo ndi Simisai mlembi, nawonso analemba kalata yawo yoneneza anthu a ku Yerusalemu kwa mfumu Aritasasita. Anayilemba motere:

Onani mutuwo Koperani




Ezara 4:8
6 Mawu Ofanana  

ndi Seva anali mlembi; ndi Zadoki ndi Abiyatara anali ansembe;


ndi Zadoki mwana wa Ahitubi, ndi Ahimeleki mwana wa Abiyatara anali ansembe, ndi Seraya anali mlembi.


Ndipo m'mene adaitana mfumu, anawatulukira Eliyakimu mwana wa Hilikiya woyang'anira nyumba ya mfumu, ndi Sebina mlembi, ndi Yowa mwana wa Asafu wolemba mbiri.


Mfumu nibweza mau kwa Rehumu chiwinda cha malamulo, ndi kwa Simisai mlembi, ndi kwa anzao otsala okhala mu Samariya, ndi otsala tsidya lino la mtsinjewo, Moni, ndi nthawi yakuti.


Ndipo masiku a Arita-kisereksesi Bisilamu, Mitiredati, Tabeele, ndi anzao otsala, analembera kwa Arita-kisereksesi mfumu ya Persiya; ndi chilembedwe chake cha kalatayo anamlemba mu Chiaramu, namsanduliza mu Chiaramu.


nalembera Rehumu chiwinda cha malamulo, ndi Simisai mlembi, ndi anzake otsala; Adinai, ndi Afarisatikai, Ataripilai, Afarisai, Aereke, Ababiloni, Asusani, Adehai, Aelamu,


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa