Ezara 4:6 - Buku Lopatulika6 Ndipo pokhala mfumu Ahasuwero, poyambira ufumu wake, analembera chowaneneza okhala mu Yuda ndi mu Yerusalemu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Ndipo pokhala mfumu Ahasuwero, poyambira ufumu wake, analembera chowaneneza okhala m'Yuda ndi m'Yerusalemu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Pamene mfumu Ahasuwero adayamba kulamulira dziko, adani aja adalemba kalata yoneneza nzika zija za ku Yuda ndi za ku Yerusalemu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Mfumu Ahasiwero atangoyamba kulamulira dzikolo, adani aja analemba kalata yoneneza anthu a Yuda ndi Yerusalemu. Onani mutuwo |