Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Ezara 4:5 - Buku Lopatulika

5 nalembera opangira atsutsane nao, nafafanize uphungu wao, masiku onse a Kirusi mfumu ya Persiya, mpaka ufumu wa Dariusi mfumu ya Persiya.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

5 nalembera opangira atsutsane nao, nafafanize uphungu wao, masiku onse a Kirusi mfumu ya Persiya, mpaka ufumu wa Dariusi mfumu ya Persiya.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

5 Adalemba akuluakulu ena kuti alepheretse cholinga chao cha pa ntchitoyo pa nthaŵi yonse ya Kirusi, mfumu ya ku Persiya, ngakhalenso mpaka pamene Dariusi, mfumu ya ku Persiya ankalamulira dzikolo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

5 Analemba alangizi ena kuti alepheretse cholinga chawo pa ntchitoyo pa nthawi yonse ya Koresi, mfumu ya ku Perisiya, ndiponso mpaka pamene Dariyo mfumu ya ku Perisiya ankalamulira dzikolo.

Onani mutuwo Koperani




Ezara 4:5
9 Mawu Ofanana  

Ndipo anachita choipa pamaso pa Yehova, monga umo anachitira a nyumba ya Ahabu; pakuti ompangira ndi iwowa, atamwalira atate wake; ndi kuonongeka kwake nkumeneko.


Momwemo inalekeka ntchito ya nyumba ya Mulungu yokhala ku Yerusalemu; nilekeka mpaka chaka chachiwiri cha ufumu wa Dariusi mfumu ya Persiya.


Pamenepo anthu a m'dziko anafoketsa manja a anthu Ayuda, nawavuta pomanga,


Ndipo pokhala mfumu Ahasuwero, poyambira ufumu wake, analembera chowaneneza okhala mu Yuda ndi mu Yerusalemu.


Koma diso la Mulungu wao linali pa akulu a Ayuda, ndipo sanawaletse mpaka mlandu unamdzera Dariusi, nabweza mau a mlanduwo m'kalata.


Koma kalonga wa ufumu wa Persiya ananditsekerezera njira masiku makumi awiri ndi limodzi; ndipo taonani, Mikaele, wina wa akalonga omveka, anadza kundithandiza; ndipo ndinakhala komweko ndi mafumu a Persiya.


Mwa iwe watuluka wina wolingalira choipa chotsutsana ndi Yehova, ndiye phungu wopanda pake.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa