Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Ezara 4:4 - Buku Lopatulika

4 Pamenepo anthu a m'dziko anafoketsa manja a anthu Ayuda, nawavuta pomanga,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

4 Pamenepo anthu a m'dziko anafoketsa manja a anthu Ayuda, nawavuta pomanga,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

4 Atamva zimenezi anthu a m'dzikomo adayamba kutayitsa mtima Ayuda, ndi kuŵachititsa mantha kuti aleke ntchito yomangayo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

4 Tsono anthu a mʼdzikomo anayamba kuchititsa ulesi anthu a ku Yuda, ndi kuwachititsa mantha kuti aleke ntchito yomangayo.

Onani mutuwo Koperani




Ezara 4:4
11 Mawu Ofanana  

Ndipo pamene Isiboseti mwana wa Saulo, anamva kuti Abinere adakafera ku Hebroni, manja ake anafooka, ndi Aisraele onse anavutika.


Ndipo anakhazika guwa la nsembe patsinde pake chifukwa cha kuopa iwo anthu a m'maikomo; nakwezera Yehova nsembe zopsereza pamenepo, nsembe zopsereza zam'mawa ndi zamadzulo.


nalembera opangira atsutsane nao, nafafanize uphungu wao, masiku onse a Kirusi mfumu ya Persiya, mpaka ufumu wa Dariusi mfumu ya Persiya.


Nati adani athu, Sadzadziwa kapena kuona mpaka talowa pakati pao, ndi kuwapha, ndi kuleketsa ntchitoyi.


Nanena iye pamaso pa abale ake ndi ankhondo a ku Samariya, nati, Alikuchitanji Ayuda ofookawa? Adzimangire linga kodi? Adzapereka nsembe kodi? Adzatsiriza tsiku limodzi kodi? Adzakometsanso miyala ya ku miunda yotenthedwa?


Pakuti anafuna onse kutiopsa, ndi kuti, Manja ao adzaleka ntchito, ndipo siidzachitika. Koma Inu, Mulungu, mulimbitse manja anga tsopano.


Ndipo akulu anati kwa mfumu, Munthu uyu aphedwetu; chifukwa analopetsa manja a anthu a nkhondo otsala m'mzinda muno, ndi manja a anthu onse, pakunena kwa iwo mau otero; pakuti munthu uyu safuna mtendere wa anthu awa, koma nsautso yao.


Koma kalonga wa ufumu wa Persiya ananditsekerezera njira masiku makumi awiri ndi limodzi; ndipo taonani, Mikaele, wina wa akalonga omveka, anadza kundithandiza; ndipo ndinakhala komweko ndi mafumu a Persiya.


Pamenepo anati, Kodi udziwa chifukwa choti ndakudzera? Ndipo tsopano ndibwerera kulimbana ndi kalonga wa Persiya; ndipo pomuka ine, taonani, adzadza kalonga wa Agriki.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa