Ezara 4:21 - Buku Lopatulika21 Mulamulire tsono kuti anthu awa aleke, ndi kuti asamange mzinda uwu, mpaka ndidzalamulira ndine. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Mulamulire tsono kuti anthu awa aleke, ndi kuti asamange mudzi uwu, mpaka ndidzalamulira ndine. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Tsono inu mulembe lamulo loŵaletsa anthu amenewo kuti asamangenso mzinda umenewo, mpaka ine nditaloleza. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Tsopano inu khazikitsani lamulo kuti anthu amenewo asiye ntchitoyo, asamangenso mzindawo mpaka ine nditalamula Onani mutuwo |