Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Ezara 2:6 - Buku Lopatulika

6 Ana a Pahatimowabu, a ana a Yesuwa ndi Yowabu, zikwi ziwiri mphambu mazana asanu ndi atatu kudza khumi ndi awiri.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

6 Ana a Pahatimowabu, a ana a Yesuwa ndi Yowabu, zikwi ziwiri mphambu mazana asanu ndi atatu kudza khumi ndi awiri.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

6 A banja la Pahatimowabu, ndiye kuti zidzukulu za Yesuwa ndi Yowabu, 2,812.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

6 zidzukulu za Pahati-Mowabu (zochokera kwa Yesuwa ndi Yowabu) 2,812

Onani mutuwo Koperani




Ezara 2:6
6 Mawu Ofanana  

Ayang'anire ichi tsono akalonga athu a msonkhano wonse, ndi onse a m'mizinda mwathu amene anadzitengera akazi achilendo abwere pa nthawi zoikika, ndi pamodzi nao akulu a mzinda wao uliwonse, ndi oweruza ake, mpaka udzatichokera mkwiyo waukali wa Mulungu wathu chifukwa cha mlandu uwu.


Ndi a ana a Pahatimowabu: Adina, ndi Kelali, Benaya, Maaseiya, Mataniya, Bezalele, ndi Binuyi, ndi Manase.


Ana a Elamu, chikwi chimodzi mphambu mazana awiri kudza makumi asanu ndi anai.


Wa ana a Pahatimowabu, Eliehoenai mwana wa Zerahiya; ndi pamodzi naye amuna mazana awiri.


Wa ana a Yowabu, Obadiya mwana wa Yehiyele; ndi pamodzi naye amuna mazana awiri mphambu khumi kudza asanu ndi atatu.


Ana a Pahatimowabu, a ana a Yesuwa ndi Yowabu, zikwi ziwiri mphambu mazana asanu ndi atatu kudza khumi limodzi ndi asanu ndi atatu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa