Ezara 2:3 - Buku Lopatulika3 ana a Parosi, zikwi ziwiri ndi zana limodzi mphambu makumi asanu ndi awiri kudza awiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 ana a Parosi, zikwi ziwiri ndi zana limodzi mphambu makumi asanu ndi awiri kudza awiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 A banja la Parosi, 2,172. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Zidzukulu za Parosi 2,172 Onani mutuwo |