Ezara 2:12 - Buku Lopatulika12 Ana a Azigadi, chikwi chimodzi mphambu mazana awiri kudza makumi awiri ndi awiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Ana a Azigadi, chikwi chimodzi mphambu mazana awiri kudza makumi awiri ndi awiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 A banja la Azigadi, 1,222. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 zidzukulu za Azigadi 1,222 Onani mutuwo |