Ezara 10:7 - Buku Lopatulika7 Nabukitsa iwo mau mwa Yuda ndi Yerusalemu kwa ana onse otengedwa ndende, kuti azisonkhana ku Yerusalemu; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Nabukitsa iwo mau mwa Yuda ndi Yerusalemu kwa ana onse otengedwa ndende, kuti azisonkhana ku Yerusalemu; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Tsono anthu adalengeza m'dziko lonse la Yuda ndi mu mzinda wa Yerusalemu, kwa onse ochokera ku ukapolo aja, kuti asonkhane ku Yerusalemu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Tsono anthu analengeza mʼdziko lonse la Yuda ndi mʼmizinda yonse ya Yerusalemu kwa onse ochokera ku ukapolo aja kuti asonkhane ku Yerusalemu. Onani mutuwo |