Estere 8:12 - Buku Lopatulika12 tsiku lomwelo, m'maiko onse a mfumu Ahasuwero, tsiku lakhumi ndi chitatu la mwezi wakhumi ndi chiwiri, ndiwo mwezi wa Adara. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 tsiku lomwelo, m'maiko onse a mfumu Ahasuwero, tsiku lakhumi ndi chitatu la mwezi wakhumi ndi chiwiri, ndiwo mwezi wa Adara. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Ayuda analoledwa kuchita zimenezi mʼzigawo zonse za Mfumu Ahasiwero pa tsiku limodzi lokha la 13 la mwezi wa 12, mwezi wa Adara. Onani mutuwo |