Estere 5:5 - Buku Lopatulika5 Niti mfumu, Mumfulumize Hamani, achitike mau a Estere. Nidza mfumu ndi Hamani ku madyerero adawakonzera Estere. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Niti mfumu, Mumfulumize Hamani, achitike mau a Estere. Nidza mfumu ndi Hamani ku madyerero adawakonzera Estere. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Mfumu inati, “Muwuzeni abwere Hamani msanga, kotero kuti tichite monga Estere wapempha.” Choncho mfumu ndi Hamani anafika kuphwando limene Estere anakonza. Onani mutuwo |