Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Estere 4:9 - Buku Lopatulika

9 Nadza Hataki, namuuza Estere mau a Mordekai.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

9 Nadza Hataki, namuuza Estere mau a Mordekai.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

9 Hataki anabwerera ndi kumufotokozera Estere zimene Mordekai ananena.

Onani mutuwo Koperani




Estere 4:9
4 Mawu Ofanana  

Pamenepo Estere ananena ndi Hataki, namtuma akauze Mordekai, ndi kuti,


Pamenepo Estere anaitana Hataki mdindo wina wa mfumu, amene idamuika amtumikire, namuuza amuke kwa Mordekai, kuti adziwe ichi nchiyani ndi chifukwa chake ninji.


Anampatsanso chitsanzo cha lamulo lolembedwa adalibukitsa mu Susa, kuwaononga, achionetse kwa Estere, ndi kumfotokozera, ndi kumlangiza alowe kwa mfumu, kumpembedza, ndi kupempherera anthu ake kwa iye.


Monga chipale chofewa m'malimwe, ndi mvula m'masika, momwemo ulemu suyenera chitsiru.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa