Estere 4:7 - Buku Lopatulika7 Ndipo Mordekai anamfotokozera zonse zidamgwera, ndi mtengo wake wa ndalama adati Hamani adzapereka m'nyumba ya chuma cha mfumu pa Ayuda, kuwaononga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Ndipo Mordekai anamfotokozera zonse zidamgwera, ndi mtengo wake wa ndalama adati Hamani adzapereka m'nyumba ya chuma cha mfumu pa Ayuda, kuwaononga. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Mordekai anamuwuza zonse zimene zinamuchitikira kuphatikizapo mtengo weniweni wa ndalama zimene Hamani analonjeza kupereka mosungira chuma cha mfumu za anthu amene adzawononge a Yuda. Onani mutuwo |