Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Estere 4:12 - Buku Lopatulika

12 Ndipo anamuuza Mordekai mau a Estere.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

12 Ndipo anamuuza Mordekai mau a Estere.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

12 Tsono Mordekai anawuzidwa mawu a Estere.

Onani mutuwo Koperani




Estere 4:12
2 Mawu Ofanana  

Akapolo onse a mfumu ndi anthu a m'maiko a mfumu adziwa kuti aliyense, ngakhale wamwamuna kapena wamkazi, akalowa kwa mfumu kubwalo la m'katimo wosaitanidwa, lamulo la pa iye ndi limodzi, ndilo kuti amuphe, akapanda mfumu kumloza ndi ndodo yachifumu yagolide kuti akhale ndi moyo; koma ine sanandiitane ndilowe kwa mfumu masiku awa makumi atatu.


Koma Mordekai anawauza ambwezere mau Estere, kuti, Usamayesa m'mtima mwako kuti udzapulumuka m'nyumba ya mfumu koposa Ayuda ena onse.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa