Estere 3:3 - Buku Lopatulika3 Ndipo anyamata a mfumu okhala m'chipata cha mfumu anati kwa Mordekai, Ulakwiranji pa lamulo la mfumu? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Ndipo anyamata a mfumu okhala m'chipata cha mfumu anati kwa Mordekai, Ulakwiranji pa lamulo la mfumu? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Kenaka atumiki a mfumu amene anali pa chipata anafunsa Mordekai kuti, “Kodi nʼchifukwa chiyani sumvera lamulo la mfumu?” Onani mutuwo |