Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Estere 2:4 - Buku Lopatulika

4 ndi namwali womkonda mfumu akhale mkazi wamkulu m'malo mwa Vasiti. Ndipo chinthuchi chinamkonda mfumu, nachita chomwecho.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

4 ndi namwali womkonda mfumu akhale mkazi wamkulu m'malo mwa Vasiti. Ndipo chinthuchi chinamkonda mfumu, nachita chomwecho.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

4 Ndipo namwali amene mfumu yakondwera naye akhale mfumukazi mʼmalo mwa Vasiti.” Mfumu inakondwera ndi uphunguwu, ndipo inachita momwemo.

Onani mutuwo Koperani




Estere 2:4
11 Mawu Ofanana  

Ndipo mauwa anamuyenerera Abisalomu, ndi akulu onse a Israele.


Ndipo mauwo anakonda mfumu ndi akalonga; ndi mfumu inachita monga mwa mau a Memukana,


Ndipo posonkhanidwa anamwali nthawi yachiwiri Mordekai anali wa m'bwalo la mfumu.


ndi mfumu aike oyang'anira m'maiko onse a ufumu wake, kuti asonkhanitse anamwali onse okongola m'chinyumba cha ku Susa, m'nyumba ya akazi; awasunge Hegai mdindo wa mfumu wosungira akazi, nawapatse zowayeretsa;


Panali Myuda m'chinyumba cha ku Susa, dzina lake ndiye Mordekai, mwana wa Yairi, mwana wa Simei, mwana wa Kisi Mbenjamini;


Koma pakufika tsiku la kubadwa kwake kwa Herode, mwana wamkazi wa Herodiasi anavina pakati pao, namkondweretsa Herode.


Chomwecho omalizira adzakhala oyamba, ndipo oyamba adzakhala omalizira.


Pakuti oitanidwa ndiwo ambiri, koma osankhidwa ndiwo owerengeka.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa