Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Estere 1:5 - Buku Lopatulika

5 Atatha masikuwa, mfumu inakonzera madyerero anthu onse okhala m'chinyumba cha ku Susa, aakulu ndi aang'ono, masiku asanu ndi awiri, ku bwalo la munda wa maluwa wa ku chinyumba cha mfumu;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

5 Atatha masikuwa, mfumu inakonzera madyerero anthu onse okhala m'chinyumba cha ku Susa, akulu ndi ang'ono, masiku asanu ndi awiri, ku bwalo la munda wa maluwa wa ku chinyumba cha mfumu;

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

5 Atatha masiku amenewa, kwa masiku ena asanu ndi awiri mfumu inakonzanso phwando la anthu onse okhala mu mzinda wa Susa kuyambira anthu olemekezeka mpaka anthu wamba ku bwalo la munda la nyumba yake yaufumu.

Onani mutuwo Koperani




Estere 1:5
4 Mawu Ofanana  

pamene anaonetsa zolemera za ufumu wake waulemu, ndi ulemerero wa ukulu wake woposa, masiku ambiri, ndiwo masiku zana limodzi mphambu makumi asanu ndi atatu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa