Eksodo 39:19 - Buku Lopatulika19 Ndipo anapanga mphete ziwiri zagolide, naziika pansonga ziwiri za chapachifuwa, m'mphepete mwake m'katimo, pa mbali ya kuefodi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Ndipo anapanga mphete ziwiri zagolide, naziika pa nsonga ziwiri za chapachifuwa, m'mphepete mwake m'katimo, pa mbali ya kuefodi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Adapanga mphete ziŵiri zagolide, nazilumikiza ku nsonga ziŵiri za chovala chapachifuwa cham'mphepete, m'kati mwake, pafupi ndi chovala cha efodi chija. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Anapanganso mphete ziwiri zagolide ndipo analumikiza ku ngodya ziwiri zamʼmunsi mwa chovala chapachifuwa, champhepete mwake, mʼkati pafupi ndi efodi ija. Onani mutuwo |