Eksodo 35:32 - Buku Lopatulika32 kulingirira ntchito zaluso, kuchita ndi golide, ndi siliva, ndi mkuwa; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201432 kulingirira ntchito zaluso, kuchita ndi golide, ndi siliva, ndi mkuwa; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa32 Amadziŵanso kulemba mapulani a ntchito zaluso ndi kugwira ntchito ndi golide, siliva ndi mkuŵa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero32 Kulemba ndondomeko ya ntchito zaluso ndi kupanga zinthu zagolide, zasiliva ndi zamkuwa, Onani mutuwo |