Eksodo 35:20 - Buku Lopatulika20 Ndipo khamu lonse la ana a Israele linachoka pamaso pa Mose. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 Ndipo khamu lonse la ana a Israele linachoka pamaso pa Mose. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Tsono Aisraele onse aja adachoka ndi kumsiya Mose. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 Kenaka gulu lonse la Aisraeli linachoka pamaso pa Mose, Onani mutuwo |